Masalmo 139:14 BL92

14 Ndikuyamikani cifukwa kuti cipangidwe canga ncoopsa ndi codabwiza;Nchito zanu nzodabwiza;Moyo wanga ucidziwa ici bwino ndithu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 139

Onani Masalmo 139:14 nkhani