23 Mundisanthule, Mulungu, nimudziwe mtima wanga;Mundiyese nimudziwe zolingalira zanga.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 139
Onani Masalmo 139:23 nkhani