4 Ndilindireni Yehova, ndisalowe m'manja mwa woipa;Ndisungeni kwa munthu waciwawa;Kwa iwo akuti akankhe mapazi anga.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 140
Onani Masalmo 140:4 nkhani