10 Ndiye amene apatsa mafumu cipulumutso:Amene alanditsa Davide mtumiki wace ku lupanga loipa.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 144
Onani Masalmo 144:10 nkhani