Masalmo 145:3 BL92

3 Yehova ndi wamkulu, nayenera kulemekezedwa kwakukuru;Ndi ukulu wace ngwosasanthulika.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 145

Onani Masalmo 145:3 nkhani