5 Wodala munthu amene akhala naye Mulungu wa Yakobo kuti amthandize,Ciyembekezo cace ciri pa Yehova, Mulungu wace;
Werengani mutu wathunthu Masalmo 146
Onani Masalmo 146:5 nkhani