13 Alemekeze dzina la Yehova;Pakuti dzina lace lokha ndi lokwezeka;Ulemerero wace uli pamwamba pa dziko lapansi ndi thambo.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 148
Onani Masalmo 148:13 nkhani