Masalmo 18:6 BL92

6 M'kusauka kwanga ndinaitana Yehova,Ndipo ndinakuwira Mulungu wanga;Mau anga anawamva m'Kacisi mwace,Ndipo mkuwo wanga wa pankhope pace unalowa m'makutu mwace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 18

Onani Masalmo 18:6 nkhani