24 Pakuti sanapeputsa ndipo sananyansidwa ndi zunzo la wozunzika;Ndipo sanambisira nkhope yace;Koma pompfuulira Iye, anamva.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 22
Onani Masalmo 22:24 nkhani