Masalmo 25:7 BL92

7 Musakumbukile zolakwa za ubwana wanga kapena zopikisana nanu:Mundikumbukile monga mwa cifundo canu,Cifukwa ca ubwino wanu, Yehova.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 25

Onani Masalmo 25:7 nkhani