Masalmo 28:3 BL92

3 Musandikoke kundicotsa pamodzi ndi oipa,Ndi ocita zopanda pace;Amene alankhula zamtendere ndi anansi ao,Koma mumtima mwao muli coipa.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 28

Onani Masalmo 28:3 nkhani