Masalmo 29:11 BL92

11 Yehova adzapatsa anthu ace mphamvu:Yehova adzadalitsa anthu ace ndi mtendere.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 29

Onani Masalmo 29:11 nkhani