Masalmo 31:19 BL92

19 Ha! kukoma kwanu ndiko kwakukuru nanga, kumene munasungira iwo akuopa Inu,Kumene munacitira iwo akukhulupirira Inu, pamaso pa ana a anthu!

Werengani mutu wathunthu Masalmo 31

Onani Masalmo 31:19 nkhani