Masalmo 31:22 BL92

22 Ndipo ine, pakutenga nkhawa, ndinati, Ndadulidwa kundicotsa pamaso panu:Komatu munamva mau a kupemba kwanga pamene ndinapfuulira kwa Inu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 31

Onani Masalmo 31:22 nkhani