Masalmo 31:9 BL92

9 Mundicitire cifundo, Yehova, pakuti ndasautsika ine:Diso langa, mzimu wanga, ndi mimba yanga, zapuwala ndi mabvuto,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 31

Onani Masalmo 31:9 nkhani