Masalmo 32:1 BL92

1 Wodala munthuyo wokhululukidwa chimo lace;Wokwiriridwa coipa cace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 32

Onani Masalmo 32:1 nkhani