5 Ndinabvomera coipa canga kwa Inu;Ndipo mphulupulu yanga sindinaibisa.Ndinati, Ndidzaululira Yehova macimo anga;Ndipo munakhululukira coipa ca kulakwa kwanga.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 32
Onani Masalmo 32:5 nkhani