Masalmo 37:34 BL92

34 Yembekeza Yehova, nusunge njira yace,Ndipo Iye adzakukweza kuti ulandire dziko:Pakudutidwa oipa udzapenya,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 37

Onani Masalmo 37:34 nkhani