Masalmo 38:12 BL92

12 Ndipo andichera misampha iwo akufuna moyo wanga;Ndipo iwo akuyesa kundicitira coipa alankhula zoononga,Nalingirira zonyenga tsiku lonse.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 38

Onani Masalmo 38:12 nkhani