19 Koma adani anga ali ndi moyo, nakhalandi mphamvu:Ndipo akundida kopanda cifukwa acuruka.
20 Ndipo iwo akubwezera coipa pa cabwinoAtsutsana nane, popeza nditsata cabwino.
21 Musanditaye, Yehova:Mulungu wanga, musakhale kutali ndi ine.
22 Fulumirani kundithandiza,Ambuye, cipulumutso canga.