1 Ndinati, Ndidzasunga njira zanga,Kuti ndingacimwe ndi lilime langa:Ndidzasunga pakamwa panga ndi cam'kamwa,Pokhala woipa ali pamaso panga.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 39
Onani Masalmo 39:1 nkhani