12 Imvani pemphero langa, Yehova, ndipo cherani khutu kulira kwanga;Musakhale cete pa misozi yanga:Pakuti ine ndine mlendo ndi Inu,Wosakhazikika, monga makolo anga onse.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 39
Onani Masalmo 39:12 nkhani