Masalmo 39:5 BL92

5 Onani, munaika masiku anga akhale monga kuyesa dzanja;Ndipo zaka zanga ziri ngati cabe pamaso panu:Indedi munthu ali yense angakhale wokhazikika, ali cabe konse.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 39

Onani Masalmo 39:5 nkhani