12 Pakuti zoipa zosawerengeka zandizinga,Zocimwa zanga zandipeza kotero kuti sindikhoza kupenya;Ziposa tsitsi la mutu wanga, ndipo wandicokera mtima.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 40
Onani Masalmo 40:12 nkhani