Masalmo 40:5 BL92

5 Inu, Yehova, Mulungu wanga, zodabwiza zanu mudazicita nzambiri,Ndipo zolingirira zanu za pa ife;Palibe wina wozifotokozera Inu;Ndikazisimba ndi kuzichula, Zindicurukira kuziwerenga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 40

Onani Masalmo 40:5 nkhani