5 Udziweramiranji moyo wanga iwe?Ndi kuzingwa m'kati mwanga?Yembekeza Mulungu, pakuti ndidzamyamikansoCifukwa ca cipulumutso ca nkhope yace.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 42
Onani Masalmo 42:5 nkhani