Masalmo 42:9 BL92

9 Ndidzati kwa Mulungu, thanthwe langa, mwandiiwala cifukwa ninji?Ndimayenderanji wakulira Cifukwa ca kundipsinja mdaniyo?

Werengani mutu wathunthu Masalmo 42

Onani Masalmo 42:9 nkhani