Masalmo 43:5 BL92

5 Udziweramiranji moyo wanga iwe?Ndi kuzingwa m'kati mwanga?Yembekeza Mulungu: pakuti ndidzamyamikanso,Ndiye cipulumutso ca nkhope yanga, ndi Mulungu wanga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 43

Onani Masalmo 43:5 nkhani