6 Mpando wacifumu wanu, Mulungu, ukhala nthawi zonse zamkamuyaya:Ndodo yacifumu ya ufumu wanu ndiyo ndodo yolunjika.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 45
Onani Masalmo 45:6 nkhani