8 Zobvala zanu zonse nza mure, ndi khonje, ndi kasya;M'zinyumba za mfumu zomanga ndi minyanga ya njobvu mwatoruka zoyimba za zingwe zokukondweretsani.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 45
Onani Masalmo 45:8 nkhani