3 Adzafika Mulungu wathu, ndipo sadzakhala cete:Moto udzanyeka pankhope pace,Ndipo pozungulira pace padzasokosera kwakukuru.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 50
Onani Masalmo 50:3 nkhani