8 Sindikudzudzula iwe cifukwa ca nsembe zako;Popeza nsembe zako zopsereza ziri pamaso panga cikhalire.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 50
Onani Masalmo 50:8 nkhani