Masalmo 51:1 BL92

1 Mundicitire ine cifundo, Mulungu,Monga mwa kukoma mtima kwanu;Monga mwa unyinji wa nsoni zokoma zanuMufafanize macimo anga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 51

Onani Masalmo 51:1 nkhani