Masalmo 52:9 BL92

9 Ndidzakuyamikani kosatha, popeza Inu munacicita ici:Ndipo ndidzayembekeza dzina lanu, pakuti ici ncokoma, pamaso pa okondedwa anu,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 52

Onani Masalmo 52:9 nkhani