Masalmo 53:5 BL92

5 Pamenepo anaopa kwakukuru, popanda cifukwa ca kuopa:Pakuti Mulungu anamwaza mafupa a iwo akuzinga iwe;Unawacititsa manyazi, pakuti Mulungu anawakaniza.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 53

Onani Masalmo 53:5 nkhani