Masalmo 55:21 BL92

21 Pakamwa pace mposalala ngati mafuta amkaka,Koma mumtima mwace munali nkhondo:Mau ace ngofewa ngati mafuta oyenga,Koma anali malupanga osololasolola.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 55

Onani Masalmo 55:21 nkhani