3 Cifukwa ca mau a mdani,Cifukwa ca kundipsinja woipa;Pakuti andisenza zopanda pace,Ndipo adana nane mumkwiyo.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 55
Onani Masalmo 55:3 nkhani