Masalmo 57:1 BL92

1 Mundicitire cifundo, Mulungu, mundicitire cifundo;Pakuti moyo wanga ukhulupirira Inu:Ndipo ndithawira ku mthunzi wa mapiko anu,Kufikira zosakazazo zidzapita.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 57

Onani Masalmo 57:1 nkhani