6 Anandichera ukonde apo ndiyenda;Moyo wanga wawerama:Anandikumbira mbuna patsogolo panga;Anagwa m'kati mwace iwo okha.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 57
Onani Masalmo 57:6 nkhani