12 Pakamwa pao acimwa ndi mau onse a pa milomo yao,Potero akodwe m'kudzitamandira kwao,Ndiponso cifukwa ca kutemberera ndi bodza azilankhula.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 59
Onani Masalmo 59:12 nkhani