16 Koma ine, ndidzayimbira mphamvu yanu;Inde ndidzayimbitsa cifundo canu mamawa:Pakuti Inu mwakhala msanje wanga,Ndi pothawirapo ine tsiku la nsautso yanga.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 59
Onani Masalmo 59:16 nkhani