2 Ku malekezero a dziko lapansi ndidzapfuulira kwa Inu, pomizika mtima wanga:Nditsogolereni ku thanthwe londiposa ine m'kutalika kwace.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 61
Onani Masalmo 61:2 nkhani