Masalmo 68:13 BL92

13 Pogona inu m'makola a zoweta,Mukhala ngati mapiko a njiwa okulira ndi siliva,Ndi nthenga zace zokulira ndi golidi woyenga wonyezimira.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 68

Onani Masalmo 68:13 nkhani