13 Koma ine, pemphero langa liri kwa Inu, Yehova, m'nyengo yolandirika;Mulungu, mwa cifundo canu cacikuru,Mundibvomereze ndi coonadi ca cipulumutso canu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 69
Onani Masalmo 69:13 nkhani