35 Pakuti Mulungu adzapulumutsa Ziyoni, nadzamanga midzi ya Yuda;Ndipo iwo adzakhala komweko, likhale lao lao.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 69
Onani Masalmo 69:35 nkhani