4 Ondida kopanda cifukwa acuruka koposa tsitsi la pamutu panga;Ofuna kunditha, ndiwo adani anga monama, ali ndi mphamvu:Pamenepo andibwezetsa cosafunkha ine.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 69
Onani Masalmo 69:4 nkhani