Masalmo 7:6 BL92

6 Ukani Yehova mu mkwiyo wanu,Nyamukani cifukwa ca ukali wa akundisautsa:Ndipo mugalamukire ine; mwalamulira ciweruzo.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 7

Onani Masalmo 7:6 nkhani