6 Inu munandigwirizizakuyambira ndisanabadwe:Kuyambira pa thupi la mai wanga wondicitira zokoma ndinu;Ndidzakulemekezani kosalekeza.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 71
Onani Masalmo 71:6 nkhani