15 Ndipo iye adzakhala ndi moyo; ndipo adzampatsa golidi wa ku Sheba;Nadzampempherera kosalekeza;Adzamlemekeza tsiku lonse.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 72
Onani Masalmo 72:15 nkhani