17 Dzina lace lidzakhala kosatha:Momwe likhalira dzuwa dzina lace lidzamvekera zidzukulu:Ndipo anthu adzadalitsidwa mwa Iye;Amitundu onse adzamucha wodala.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 72
Onani Masalmo 72:17 nkhani